1: (krazie g) Fans ngati ganja ndikupotayi nayo yambirimbiri ili nthumba mwa 3 quarter'yi (ah iwe zimenezo) eish oh ayi (Tikukamba za chilembwe) oh n'dala wa Ndimamusaka ngati amene anamupha Ndikampeza celebration pali kudumphadumpha Ndimayesesa daily nthumbamu Nde dolla zosaka ku kuchita kutuwa mbu I ronaldo, messi money, nike, addidas ili nkhani ya dollar ndipange add basi Make mad thousands and call em G's I make crazy and call em amazing me Ndikudya paper koma akumva kuwawa ndi Esther lero koma mawa ndi Tina Siine looks ndine nkhwangwa Koma akazi ndi nkhuni Chifukwa cha wanga
(revolver) Ndikusaka m'busa uja in a khakhi If you see him mundiwuze ali kuti No homo but i love him a choir Sindigwanda chilembwe olo Wakale, wokwinyika wong'ambika Olo ali ine ndimuyanika Sinditha kuphika but damn Funsa mng'ono wa yanga, ndikudya moola Coz i stay on my grind like am to Kufuna jc ndili mu form 2 Thats john chilembwe, wa kamuzu wa Gomani, best friend wanga uyu Ngongole sindibweza, ndimasowa wandikwana ndikulowela ku Dowa Alipo ma man onditchesa Lero akafika pa yard
(tanaposi & G) John John john chilembwe John john chilembwe uyu Akupoilira chilembwe
2: (martse) Ma heroe ndimaasaka john chilembwe And now i'm switching gears nduhasa banda Having is an option all i had to do is choose nde sindikhala mmaluzi This no lie John chilembwe ngwa china, wameta mohawk, wavala tie Wa ine ndi new for zibagi, dubai Ndine ndi kale nde ndimangokhala high Martse ndi mfana wotentha nde palibe nyo Ndine mtumbuka wosamba mphwanga, you know Nde mukamakambakamba za chilembweyo ali ngati dstv, so much more You dig
(hypa) Dolla ndizama looks ndiyeno fans imangokongola Fans imabwela kuzangokongola Dolla koma ine ndili phe Iwe zako kungothoka tulo ndiliphe kunenepa nde ndikungodya zi money Ku chipatala andiwuza ndisazimane Kuthoka ndi chilembwe timatchila mwa dolla zimathoka iwe zako nzachibwibwi I'm sick with the money dolla zanga Ndinkona ndikazimva zikufwenthila Anijo ndimangokanda ngati Bongo man Koma kundipempha ndimangokana Ntaba man za chilembwezi zilibe chibale Olo Faith alibe chibale Dolla zanga zimathokadi, noise Iwe zako ndekuti wagwetsa ma coins (back to chorus)
3:(judagaga) I keep it old school, chilembwe yekha yekha Kamuzu ali bho nthumba akumachepa Ndikasanja ndimafuna fans idziwe Mahope n'nawathoka nawonso adiwe Get his face on a note nde ndizamulora Dead got my number coz dolla zikundikhola I get money by all means even change chaku Chilling with dead people why my flow is mad sicker Ndimamukonda john chilembwe, you can call me Cause when i have him in my i'm sipping ciders In love with black man in a khakhi suit Siine mzungu koma ndimamuhanta ndi mifuti My account got much figure kuposa money yaku Malawi, john chilembwe wa magazi Get my money in my bra ngati sungandibele kuti HUH nanenso ndizamufele (back to chorus)