1: (krazie g) Fans ngati ganja ndikupotayi Ndili nayo yambirimbiri ili mwa 3 quarter'yi (ah iwe zimenezo) eish oh ayi (Tikukamba za chilembwe) oh n'dala wa ngati azungu amene anamupha Ndikampeza pali ponse kudumphadumpha daily apezeke nthumbamu Nde dolla zosaka ku Lilongwe kuchita mbu I ronaldo, messi money, nike, addidas Ngati ili nkhani ya dollar add basi Make mad thousands and call em G's I make crazy millions and call em me Ndikudya paper koma akumva kuwawa ndi Ndikudya Esther lero koma mawa ndi Siine wama looks nkhwangwa Koma akazi ndi nkhuni Chifukwa cha wanga
(revolver) m'busa uja in a khakhi suit If you see him chonde ali kuti No but i love him like a choir Sindigwanda olo atakhala Wakale, ngakhale wong'ambika Olo ali wonyowa ine Sinditha kuphika but damn Funsa wa bebi yanga, ndikudya moola Coz i stay on my like am s'possed to Kufuna jc ndili mu form 2 Thats john chilembwe, mng'ono wa wa Gomani, best friend wanga uyu Ngongole sindibweza, ndimasowa Mzinda wandikwana ndikulowela ku ambiri ma man onditchesa Lero pa yard sandipeza
(tanaposi & G) John chilembwe Jo-jo john chilembwe Amapoilira john uyu john chilembwe
2: (martse) Ma heroe ndimaasaka chilembwe ndiwoyamba And now i'm gears nduhasa kamuzu banda Having is an option all i had to do is choose nde sindikhala mmaluzi This no lie John chilembwe ngwa china, wameta mohawk, wavala tie Wa ine ndi brand new for zibagi, Ndine ndi kale nde ndimangokhala high Martse ndi mfana nde palibe akuti nyo Ndine mtumbuka wosamba mphwanga, you already Nde mukamakambakamba za john Waine ali ngati dstv, so much You dig
(hypa) Dolla zanga ndizama looks fans imangokongola Fans yakunyasa imabwela Dolla koma ine ndili phe Iwe zako kungothoka uwone tulo Ndikufuna kunenepa nde zi money Ku andiwuza ndizidya ndisazimane Kuthoka ndi chilembwe mwa kathithi Ngati dolla zimathoka iwe zako I'm sick the money dolla zanga zingofwenthila ndimaziblowa ndikazimva zikufwenthila Anijo kundiyabwa ndimangokanda Bongo man kundipempha ndimangokana ngati Ntaba man Nkhani za chilembwezi zilibe Olo Faith zamakwachazi chibale Dolla zanga zimathokadi, zimapanga Iwe kusokosa ndekuti wagwetsa ma coins (back to chorus)
3:(judagaga) I keep it old school, chilembwe yekha yekha Kamuzu ali bho nthumba akumachepa dolla ndimafuna fans idziwe Mahope n'nawathoka nawonso adiwe Get his face on a bank nde ndizamulora Dead people got my number coz dolla I get money by all means even change msika Chilling with dead people thats why my is mad sicker Ndimamukonda john chilembwe, you can call me Cause when i have him in my pockets i'm ciders In love with this black man in a khakhi Siine mzungu koma nane ndimamuhanta ndi My account got much kuposa akazi money yaku Malawi, john chilembwe wa magazi Get my money in my bra ngati recka kuti HUH nanenso ndizamufele (back to chorus)